Paulo Ndi Sila
Paulo ndi sila Anapemphera
Paulo ndi sila Anapemphera
Makomo a ndende Anatseguka
Makomo a ndende Anatseguka
Moyo wanga Moyo wanga
Moyo wanga Sangalala
Mukafuna kuyimba
Muyimbe ndi Yesu
Mukafuna kukondwa
Mukondwe ndi Yesu
Home